Single
[Chorus]
Ndikavunga Text Umachedwa kuyankha
Ukavunga Message Pompo Ndimayankha
Ndikaimba Phone Ngati Sukufuna Kuyankha
Ngati Sukufila Unaka Talka Ndizingoyaka
Gangster ali Single!
Bola Ndingokhala Single
Ndizingoimba Nyimbo
Ya Gangster ali single
[Verse]
Umangot Vepi Bwanji Sungatenge Tchuthi
Ndagwila phone Yako wazizidwa ulibe Juzi?
Zosathoka Zomwe ndalakwisazo Ndizachimidzi
Ndili Serious siza Lucious koma play me si Jacuzzi
Unena Bwanji kuti You With me,when u Texting other Niggas
Naneso Sindingasibise Ndatopa with your Shenanigans
Kumandiika Ntika
Koma Uli Pa Nsika
Ine ndi Business Man
Zokwera ndimazitsika
Mwina ukufuna G wabanja
Or ungofuna mwana
Koma Mnakuuza kale kuti udekhe ndingo Hasa
Ndiwe Mkazi wa Trappa
Ndizakupasa Ma Pasa
Ndikupasa Mapasa
Ndizakuoasa Mapasa
Ndizakupasa mapasa
Ukakwiya simandimafila bho ndipange admit
I like it when we cool ngati Salifornia Breeze
Ma babe ena onse basi Ndawapanga Delеte
Pachi G i'm just Trynna Show you kuti you tha one for me Koma
[Chorus]
Ndikavunga Tеxt Umachedwa kuyankha
Ukavunga Message Pompo Ndimayankha
Ndikaimba Phone Ngati Sukufuna Kuyankha
Ngati Sukufila Unaka Talka Ndizingoyaka
Gangster ali Single!
Bola Ndingokhala Single
Ndizingoimba Nyimbo
Ya Gangster ali single