Back to Sender (feat. Kell Kay, Eli & Teddy)

madalitso kantema

Yeeeh ya
Phone amazangova hello
Man nkazi uja lero
Zomwe akupanga ndi mbola
Mamuna wina aliyese angolola
Munkati mwapeza ka girl
Koma Mwazinamiza siza ngelo
Koma zachimwana
Zachibwana mungonamizana
Back to sender
Sender ayeeee, aah ayeh
Za Ine ndi nkazi wanga
Ayanganila ndi ambuye
Back to sender
Sender ayeeee, ahh ayeh
Zomwe zikanike ndiza inu ndi akwanuwo
Back to sender

Is the fact that we balling
Or you hate the fact she's my darling
Just becouse we shinning
Mpaka kumapeka nkhani
Back to sender
Nkazi wanga aise soyendayenda
Mukapitiliza nzakugenda
Mutijeda breda nzosayenda ena akathela kujahena
Zomwe mukupangazo ndudziwa kale
Basi kubwela kufuna kutitchela ndale
Cholinga nkazi wanga ndimutaye
Koma mukunama nafe ma guye
Wachitemwa wane, true love Iwe
Nkazi wanga tisamavele
Wachitemwa wane, true love Iwe
Nkazi wanga tisamavele

Phone amazangova hello
Man nkazi uja lero
Zomwe akupanga ndi mbola
Mamuna wina aliyese angolola
Munkati mwapeza ka girl
Koma Mwazinamiza siza ngelo
Koma zachimwana
Zachibwana mungonamizana
Back to sender
Sender ayeeee, aah ayeh
Za Ine ndi nkazi wanga
Ayanganila ndi ambuye
Back to sender
Sender ayeeee, ahh ayeh
Zomwe zikanike ndiza inu ndi akwanuwo
Back to sender

Komwe tinakumana inu kunalibeko
Nafusila inu kunalibeko
Chonde ndisiyileni nasibeko
Anandipatsa ndi abuye kuti eko
So we take over
So we like queen b and hova
Like Mr eazi I tell her leg over
Shes the only one I can't get over
Zomwe mukupangazo ndudziwa kale
Basi kubwela kufuna kutitchela ndale
Cholinga nkazi wanga ndimutaye
Koma mukunama nafe ma guye
Wachitemwa wane, true love Iwe
Nkazi wanga tisamavele
Wachitemwa wane, true love Iwe
Nkazi wanga tisamavele

Phone amazangova hello
Man nkazi uja lero
Zomwe akupanga ndi mbola
Mamuna wina aliyese angolola
Munkati mwapeza ka girl
Koma Mwazinamiza siza ngelo
Koma zachimwana
Zachibwana mungonamizana
Back to sender
Sender ayeeee, aah ayeh
Za Ine ndi nkazi wanga
Ayanganila ndi ambuye
Back to sender
Sender ayeeee, ahh ayeh
Zomwe zikanike ndiza inu ndi akwanuwo
Back to sender

Wissenswertes über das Lied Back to Sender (feat. Kell Kay, Eli & Teddy) von Charisma

Wer hat das Lied “Back to Sender (feat. Kell Kay, Eli & Teddy)” von Charisma komponiert?
Das Lied “Back to Sender (feat. Kell Kay, Eli & Teddy)” von Charisma wurde von madalitso kantema komponiert.

Beliebteste Lieder von Charisma

Andere Künstler von New Age